Mateyu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 244 Nsanja ya Olonda,1/15/1999, ptsa. 25-2612/15/1989, tsa. 8
23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+