Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’? Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:42 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 246-247
42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?