Mateyu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 3
2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+