Mateyu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi mbiri za nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha. Pakuti zimenezi ziyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+
6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi mbiri za nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha. Pakuti zimenezi ziyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+