-
Mateyu 28:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mwadzidzidzi Yesu anakumana nawo n’kunena kuti: “Moni amayi!” Pamenepo iwo anafika pafupi ndi kugwira mapazi ake ndi kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.
-