Maliko 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhalenso anthu ambiri ochokera ku Yerusalemu, ku Idumeya, kutsidya la Yorodano, ndi m’madera a Turo+ ndi Sidoni, anamva zonse zimene iye anali kuchita, ndipo anakhamukira kwa iye.
8 Ngakhalenso anthu ambiri ochokera ku Yerusalemu, ku Idumeya, kutsidya la Yorodano, ndi m’madera a Turo+ ndi Sidoni, anamva zonse zimene iye anali kuchita, ndipo anakhamukira kwa iye.