Maliko 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndipo madokotala+ ambiri anam’chititsa kumva zopweteka zambiri. Iye anawononga chuma chake chonse koma osapindula kanthu, m’malomwake matendawo ankangokulirakulira.
26 ndipo madokotala+ ambiri anam’chititsa kumva zopweteka zambiri. Iye anawononga chuma chake chonse koma osapindula kanthu, m’malomwake matendawo ankangokulirakulira.