Maliko 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 118 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 22
39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+