Maliko 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, iye anadabwa kuona kuti anthuwo analibe chikhulupiriro. Ndipo anazungulira m’midzi yapafupi akuphunzitsa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, tsa. 26
6 Ndithudi, iye anadabwa kuona kuti anthuwo analibe chikhulupiriro. Ndipo anazungulira m’midzi yapafupi akuphunzitsa.+