Maliko 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atadziyeretsa mwa kudziwaza madzi. Palinso miyambo ina yambiri+ imene anailandira ndipo akuisunga, monga kuviika makapu, mitsuko ndi ziwiya zamkuwa m’madzi+ . . . Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,6/15/1997, tsa. 1310/15/1989, tsa. 311/15/1989, tsa. 11
4 Akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atadziyeretsa mwa kudziwaza madzi. Palinso miyambo ina yambiri+ imene anailandira ndipo akuisunga, monga kuviika makapu, mitsuko ndi ziwiya zamkuwa m’madzi+ . . .