Maliko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu ndi kulowa m’thupi mwake chimene chingaipitse munthu, koma zotuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+
15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu ndi kulowa m’thupi mwake chimene chingaipitse munthu, koma zotuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+