Maliko 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma poyankha mayiyo ananena kuti: “Inde mbuyanga, komabe tiagalu timadya nyenyeswa+ za anawo pansi pa tebulo.”+
28 Koma poyankha mayiyo ananena kuti: “Inde mbuyanga, komabe tiagalu timadya nyenyeswa+ za anawo pansi pa tebulo.”+