Maliko 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nthawi yomweyo bambo wa mwanayo anafuula ndi kunena kuti: “Chikhulupiriro ndili nacho! Limbitsani chikhulupiriro changa!”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:24 Nsanja ya Olonda,9/15/1991, ptsa. 14-15
24 Nthawi yomweyo bambo wa mwanayo anafuula ndi kunena kuti: “Chikhulupiriro ndili nacho! Limbitsani chikhulupiriro changa!”+