Maliko 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano atalowa m’nyumba, ophunzira ake anayamba kumufunsa paokha kuti: “N’chifukwa chiyani ife tinalephera kuutulutsa?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 147 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 8
28 Tsopano atalowa m’nyumba, ophunzira ake anayamba kumufunsa paokha kuti: “N’chifukwa chiyani ife tinalephera kuutulutsa?”+