Maliko 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo anamuyankha kuti: “Mutilole kuti mmodzi wa ife adzakhale kudzanja lanu lamanja, ndipo wina adzakhale kumanzere kwanu mu ulemerero wanu.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:37 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 228-229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
37 Iwo anamuyankha kuti: “Mutilole kuti mmodzi wa ife adzakhale kudzanja lanu lamanja, ndipo wina adzakhale kumanzere kwanu mu ulemerero wanu.”+