Maliko 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:38 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2020, tsa. 14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+
10:38 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2020, tsa. 14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8