Maliko 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso, munthu adzapereka m’bale wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake,+ ndi ana adzaukira makolo awo ndi kuwaphetsa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:12 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 27
12 Komanso, munthu adzapereka m’bale wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake,+ ndi ana adzaukira makolo awo ndi kuwaphetsa.+