Maliko 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anatenga kapu ndi kuyamika, n’kuipereka kwa iwo, ndipo onse anamwa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:23 Nsanja ya Olonda,7/1/1990, tsa. 9