Maliko 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi yomweyo, mawu adakali m’kamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira ake 12 aja, anafika limodzi ndi khamu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi alembi ndi akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:43 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
43 Nthawi yomweyo, mawu adakali m’kamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira ake 12 aja, anafika limodzi ndi khamu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi alembi ndi akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+