Luka 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Yesu—Ndi Njira, tsa. 30 Yesaya 1, ptsa. 399-401
3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+