Luka 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+
14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+