Luka 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi inayake khamu la anthu linali kumvetsera pamene Yesu anali kuphunzitsa mawu a Mulungu m’mphepete mwa nyanja ya Genesarete.*+ Kenako anthuwo anayamba kumupanikiza.
5 Nthawi inayake khamu la anthu linali kumvetsera pamene Yesu anali kuphunzitsa mawu a Mulungu m’mphepete mwa nyanja ya Genesarete.*+ Kenako anthuwo anayamba kumupanikiza.