Luka 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa, kuti: “Ndani ameneyu kuti azinyoza Mulungu chonchi?+ Winanso ndani amene angakhululukire machimo? Si Mulungu yekha kodi?”+
21 Pamenepo alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa, kuti: “Ndani ameneyu kuti azinyoza Mulungu chonchi?+ Winanso ndani amene angakhululukire machimo? Si Mulungu yekha kodi?”+