Luka 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero anthu anabwera kudzaona zomwe zachitikazo. Atafika kwa Yesu anapeza munthu amene anam’tulutsa ziwanda uja atakhala pansi pafupi ndi Yesu. Anamupeza atavala bwino komanso maganizo ake ali bwinobwino, ndipo iwo anachita mantha.+
35 Zitatero anthu anabwera kudzaona zomwe zachitikazo. Atafika kwa Yesu anapeza munthu amene anam’tulutsa ziwanda uja atakhala pansi pafupi ndi Yesu. Anamupeza atavala bwino komanso maganizo ake ali bwinobwino, ndipo iwo anachita mantha.+