Luka 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano pamene amenewa anali kulekana naye, Petulo anauza Yesu kuti:+ “Mlangizi, ndi bwino kuti ife tizikhala pano. Choncho timange mahema atatu, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.” Koma iye sanali kuzindikira zimene anali kunena. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 144 Tsanzirani, tsa. 194 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 271/1/1988, tsa. 8
33 Tsopano pamene amenewa anali kulekana naye, Petulo anauza Yesu kuti:+ “Mlangizi, ndi bwino kuti ife tizikhala pano. Choncho timange mahema atatu, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.” Koma iye sanali kuzindikira zimene anali kunena.
9:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 144 Tsanzirani, tsa. 194 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 271/1/1988, tsa. 8