Luka 9:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense wolandira mwana wamng’ono uyu m’dzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine walandiranso amene anandituma ine.+ Pakuti aliyense wokhala ngati wamng’ono+ pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 149 Nsanja ya Olonda,11/15/2012, ptsa. 15-16, 17-183/15/2008, tsa. 42/1/1988, tsa. 99/15/1986, tsa. 273/1/1987, tsa. 14
48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense wolandira mwana wamng’ono uyu m’dzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine walandiranso amene anandituma ine.+ Pakuti aliyense wokhala ngati wamng’ono+ pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu.”+
9:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 149 Nsanja ya Olonda,11/15/2012, ptsa. 15-16, 17-183/15/2008, tsa. 42/1/1988, tsa. 99/15/1986, tsa. 273/1/1987, tsa. 14