Luka 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma wina wamphamvu kuposa iyeyu+ akabwera n’kumugonjetsa,+ amamulanda zida zake zonse zimene amadalira, ndipo katundu amene wamulanda, amamugawa kwa ena. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 176 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, tsa. 8
22 Koma wina wamphamvu kuposa iyeyu+ akabwera n’kumugonjetsa,+ amamulanda zida zake zonse zimene amadalira, ndipo katundu amene wamulanda, amamugawa kwa ena.