Luka 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 3112/1/1988, tsa. 8
28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja.