Luka 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso, monga zinachitikira m’masiku a Nowa,+ zidzachitikanso chimodzimodzi m’masiku a Mwana wa munthu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:26 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 218-219 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, tsa. 19
26 Komanso, monga zinachitikira m’masiku a Nowa,+ zidzachitikanso chimodzimodzi m’masiku a Mwana wa munthu.+