Luka 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 kuti: “Mphunzitsi, Mose+ anatilembera kuti, ‘Ngati munthu wamwalira n’kusiya mkazi amene sanabereke naye ana, m’bale wake+ atenge mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana mwa mkaziyo.’+
28 kuti: “Mphunzitsi, Mose+ anatilembera kuti, ‘Ngati munthu wamwalira n’kusiya mkazi amene sanabereke naye ana, m’bale wake+ atenge mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana mwa mkaziyo.’+