Luka 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anamasula+ munthu woponyedwa m’ndende pa mlandu woukira boma ndi kupha munthu, amenenso anthuwo anapempha kuti amumasule. Koma Yesu anamupereka m’manja mwawo kuti zofuna zawo zichitike.+
25 Iye anamasula+ munthu woponyedwa m’ndende pa mlandu woukira boma ndi kupha munthu, amenenso anthuwo anapempha kuti amumasule. Koma Yesu anamupereka m’manja mwawo kuti zofuna zawo zichitike.+