Yohane 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho iye anawauzanso kuti: “Ine ndikuchoka ndipo mudzandifunafuna,+ koma mudzafabe m’tchimo lanu.+ Kumene ine ndikupita inu simungathe kukafikako.”
21 Choncho iye anawauzanso kuti: “Ine ndikuchoka ndipo mudzandifunafuna,+ koma mudzafabe m’tchimo lanu.+ Kumene ine ndikupita inu simungathe kukafikako.”