Yohane 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 164 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, tsa. 8
41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”