Yohane 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano khamu lalikulu la Ayuda linadziwa kuti Yesu ali kumeneko. Choncho linafika, osati chifukwa cha Yesu yekha ayi, komanso kuti lidzaone Lazaro, amene iye anamuukitsa kwa akufa.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:9 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, tsa. 32
9 Tsopano khamu lalikulu la Ayuda linadziwa kuti Yesu ali kumeneko. Choncho linafika, osati chifukwa cha Yesu yekha ayi, komanso kuti lidzaone Lazaro, amene iye anamuukitsa kwa akufa.+