Yohane 13:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Petulo anafunsanso kuti: “Ambuye, n’chifukwa chiyani sindingakutsatireni padakali pano? Ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha inu.”+
37 Petulo anafunsanso kuti: “Ambuye, n’chifukwa chiyani sindingakutsatireni padakali pano? Ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha inu.”+