Yohane 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ndalankhula zimenezi kwa inu m’mafanizo.+ Nthawi ikubwera pamene sindidzalankhulanso ndi inu m’mafanizo, koma ndidzakuuzani za Atate m’njira yosavuta kumva.
25 “Ndalankhula zimenezi kwa inu m’mafanizo.+ Nthawi ikubwera pamene sindidzalankhulanso ndi inu m’mafanizo, koma ndidzakuuzani za Atate m’njira yosavuta kumva.