-
Yohane 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Pamenepo Yesu anatulukira panja, atavala chisoti chachifumu chaminga chija ndi malaya akunja ofiirira. Ndipo Pilato anati: “Taonani! Mwamuna uja ndi uyu!”
-