Yohane 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yesu anafunsa mayiyo kuti: “Mayi iwe, n’chifukwa chiyani ukulira? Kodi Ukufuna ndani?”+ Poganiza kuti ndi wosamalira mundawo, iye anamuyankha kuti: “Bambo, ngati mwamuchotsa ndinu, ndiuzeni chonde kumene mwamuika, ndipo ine ndikamutenga.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:15 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo,
15 Ndiyeno Yesu anafunsa mayiyo kuti: “Mayi iwe, n’chifukwa chiyani ukulira? Kodi Ukufuna ndani?”+ Poganiza kuti ndi wosamalira mundawo, iye anamuyankha kuti: “Bambo, ngati mwamuchotsa ndinu, ndiuzeni chonde kumene mwamuika, ndipo ine ndikamutenga.”