Machitidwe 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anasonkhana pamodzi kuti achite zimene inu munaneneratu. Zimenezi zinachitika chifukwa inu muli ndi mphamvu komanso chifukwa chakuti zinali zogwirizana ndi chifuniro chanu.+
28 Iwo anasonkhana pamodzi kuti achite zimene inu munaneneratu. Zimenezi zinachitika chifukwa inu muli ndi mphamvu komanso chifukwa chakuti zinali zogwirizana ndi chifuniro chanu.+