Machitidwe 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno panafika amuna ena a gulu lotchedwa Sunagoge wa Omasulidwa, ndi ena a ku Kurene, a ku Alekizandiriya,+ komanso ena ochokera ku Kilikiya+ ndi ku Asia, kudzatsutsana ndi Sitefano. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 47 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 16
9 Ndiyeno panafika amuna ena a gulu lotchedwa Sunagoge wa Omasulidwa, ndi ena a ku Kurene, a ku Alekizandiriya,+ komanso ena ochokera ku Kilikiya+ ndi ku Asia, kudzatsutsana ndi Sitefano.