Machitidwe 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:32 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 8
32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+