Machitidwe 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atatuluka m’madzimo, mzimu wa Yehova unachotsa Filipo mwamsanga pamalopo,+ ndipo nduna ija sinamuonenso, koma inapitiriza ulendo wake ikusangalala.
39 Atatuluka m’madzimo, mzimu wa Yehova unachotsa Filipo mwamsanga pamalopo,+ ndipo nduna ija sinamuonenso, koma inapitiriza ulendo wake ikusangalala.