Machitidwe 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita m’dziko la Ayuda ndi mu Yerusalemu momwe. Koma iwo anamupha mwa kumupachika pamtengo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:39 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 28
39 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita m’dziko la Ayuda ndi mu Yerusalemu momwe. Koma iwo anamupha mwa kumupachika pamtengo.+