Machitidwe 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:45 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 72
45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+