Machitidwe 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:41 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 136/1/1991, tsa. 22
41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+