Machitidwe 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno wansembe wa Zeu, amene kachisi wake anali pafupi kunja kwa mzindawo, anabweretsa ng’ombe zamphongo ndi nkhata zamaluwa kuzipata. Iye pamodzi ndi khamu la anthulo anali kufuna kupereka nsembe.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:13 Nsanja ya Olonda,5/15/1990, tsa. 25
13 Ndiyeno wansembe wa Zeu, amene kachisi wake anali pafupi kunja kwa mzindawo, anabweretsa ng’ombe zamphongo ndi nkhata zamaluwa kuzipata. Iye pamodzi ndi khamu la anthulo anali kufuna kupereka nsembe.+