Machitidwe 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atalengeza uthenga wabwino mumzinda umenewo ndi kuphunzitsa anthu angapo kuti akhale ophunzira,+ anabwerera ku Lusitara, ku Ikoniyo ndi ku Antiokeya.
21 Atalengeza uthenga wabwino mumzinda umenewo ndi kuphunzitsa anthu angapo kuti akhale ophunzira,+ anabwerera ku Lusitara, ku Ikoniyo ndi ku Antiokeya.