Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,11/1/2015, ptsa. 13-149/15/2014, tsa. 13
22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+