Machitidwe 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ali m’sunagoge anayamba kukambirana ndi Ayuda+ ndi anthu ena opembedza Mulungu. Ndipo tsiku ndi tsiku analinso kukambirana ndi anthu amene anali kuwapeza pamsika.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 140-141 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 18
17 Choncho ali m’sunagoge anayamba kukambirana ndi Ayuda+ ndi anthu ena opembedza Mulungu. Ndipo tsiku ndi tsiku analinso kukambirana ndi anthu amene anali kuwapeza pamsika.+