Machitidwe 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudzana ndi zinthu zimenezo.+ Ndiyeno anawauza kuti: “Amuna inu, mukudziwa bwino kuti chuma chathu chimachokera m’ntchito imeneyi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 158
25 Choncho Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudzana ndi zinthu zimenezo.+ Ndiyeno anawauza kuti: “Amuna inu, mukudziwa bwino kuti chuma chathu chimachokera m’ntchito imeneyi.+